Ndimakukonda

Lyrics: Ganizani Chiwaya Music: Ganizani Chiwaya Ohooo wooo Owooo Hooo Ebel Gaxybo you know Ndimakukonda honey iwe okay Owuwooo ndimakukonda yah babe it's me again eheee ndimakukonda okay
Ndati ndikuwuze ndima kukonda ndimtima wanga wonse Ndimakukonda Nditsimikizire umandakonda Kuyambira kale ndinkakukonda Palibe kusintha ndidzakukonda Mpakana kale kale ndidzakukonda Tatiye kwathu iweeee
Ndimakukonda babe Ngithanda wena wedwa Ndimakukonda honey owuwuwoo Ngithanda wena wedwa Ndimtima wanga wonse Nhliziyo Yami yonke Ndimakukonda honey Oowwww Ngithanda wena wedwa
Ukamati umandakonda ine kumtimaku myaaaa Iwe ndi ine together mpaka mwana alire Ng'aaaa tsiku loyamba ntangokuwona mpaka diso langa ng'ala Nkuwona sindina chedwe nangopanga zongo mara Koma usapusisike nzama social media Ngadzadzese mpungwempungwe banja lathu Liliya Ungadzawone Zina m'menemo nkuyamba kusilira Basi mtima kukopeka ineyo nkundisiya Asakupusitse mayoo ndi mbatcha zobwereka Anabwera ndiyongonama kuti anali ku Amereka Koma amadzangokuthawa ukagwetsa bereka Kusiya ukutuwa ukusowa mchereka yooo I don't wanna loose whole my life I will spend with you am ready to die for you I swear I will never cheat on you It's me again
Ndimakukonda babe Ngithanda wena wedwa Ndimakukonda honey owuwuwoo Ngithanda wena wedwa Ndimtima wanga wonse Nhliziyo Yami yonke Ndimakukonda honey Oowwww Ngithanda wena wedwa
Ngakhale zokoma zinga churukee Chikondi changa babe nchopanda malire Monga kaduwa kumawa kachiwalire Tandilora babe ayi ndiku file Tatiye kwanu honey akandione Popeza kwathu honey amakukonda Tatiye kwathu iwe