Lyrics: Paul Kandonga
Music: Paul Kandonga
They told me
Love is not for everybody
With you I just wanna
Enjoy this moment
Some people
Just don't wanna see me happy
I wanna feel this moment
Eti, olo undikonde uzandisiyabe
Sumandikonda umafuna money
Zosandikhuza kaya ufuna ndife
I wanna feel this moment
Sakufila ngati ife
Asiye athoke baby
Sakunjoya ngati ife
Ngati ifeyo, ngati ifeyo
Sakunjoya ngati ife
Ngati ife
Asiye athoke baby
Sakufila ngati ife
Ngati ifeyo mmm
Ngati iwe ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ndi ine, ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ndi ine, ndi ine
Eeh, natural hair sufuna weave
The way that you whine
Ndi big league
Enawa afuna apange compete
Koma iweyo,
You got me complete
Darling
Natural hair sufuna weave
The way that you whine
Ndi big league
Enawa afuna apange compete
Koma iweyo,
You got me complete
Darling
Amakondana koma iwowo si ife
We love each other
like nobody's business
Umandipasa everything
I'm wanting
I'm gonna give you my life
Sakufila ngati ife
Asiye athoke baby
Sakunjoya ngati ife
Ngati ifeyo, ngati ifeyo
Sakunjoya ngati ife
Ngati ife
Asiye athoke baby
Sakufila ngati ife
Ngati ifeyo mmm
Ngati iwe ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ndi ine, ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ngati iwe ndi ine
Ndi ine, ndi ine