Good Life

Mtima Umakoma Kutsekemela ahh Zomwe Umachita Sumaseleula aah Ngati Kutulo Zomwe Umachita Nzogometsa aah Mwina Sumadziwa Ndiwe Moyo Wanga Unakondetsa
Ukamati Zako Zonse Ndi Ine eeh Zanga Zonse Ndizako Paja Unati Singandisiye eeh Supanga Chipako
Ndiwe Moyo Wanga Unawina aah Nkhope yako Imakana Tsinya aah
Umandipangitsa Ine Kufila Good Life aah Umandipangitsa Ine Kufila Good Life aah Dziwa Umandipangitsa Ine Kufila Good Life aah Umandipangitsa Ine Kufila Good Life aah ooh
Poti Ndiwe Mkazi Wanga Mzanga aah Susintha Mawanga aah Matama Onsewa Nkani Yake Ndi Iweyo Ku Akazi Onsewa Ine Ndisankha Iweyo